Oweruza 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ehudi atamwalira, Aisiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+