Oweruza 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Yehova anawapereka* kwa Yabini mfumu ya ku Kanani,+ amene ankalamulira ku Hazori. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Sisera, ndipo ankakhala ku Haroseti-ha-goimu.+
2 Choncho Yehova anawapereka* kwa Yabini mfumu ya ku Kanani,+ amene ankalamulira ku Hazori. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Sisera, ndipo ankakhala ku Haroseti-ha-goimu.+