Oweruza 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aisiraeli anayamba kulirira Yehova+ chifukwa Yabini anawapondereza kwambiri+ kwa zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali komanso zakuthwa.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2017, tsa. 29
3 Aisiraeli anayamba kulirira Yehova+ chifukwa Yabini anawapondereza kwambiri+ kwa zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali komanso zakuthwa.+