Oweruza 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye ankakhala pansi pa mtengo wake,* wa kanjedza pakati pa mzinda wa Rama+ ndi wa Beteli,+ mʼdera lamapiri la Efuraimu ndipo Aisiraeli ankapita kwa iye kuti akawaweruze.
5 Iye ankakhala pansi pa mtengo wake,* wa kanjedza pakati pa mzinda wa Rama+ ndi wa Beteli,+ mʼdera lamapiri la Efuraimu ndipo Aisiraeli ankapita kwa iye kuti akawaweruze.