Oweruza 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndidzabweretsa kwa iwe kumtsinje* wa Kisoni,+ Sisera mkulu wa gulu lankhondo la Yabini, pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake ndipo ndidzamʼpereka mʼmanja mwako.’”+
7 Ine ndidzabweretsa kwa iwe kumtsinje* wa Kisoni,+ Sisera mkulu wa gulu lankhondo la Yabini, pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake ndipo ndidzamʼpereka mʼmanja mwako.’”+