Oweruza 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Debora anayankha kuti: “Tipitiradi limodzi. Koma ulemerero sukhala wako pa nkhondo imeneyi, chifukwa Yehova adzapereka Sisera mʼmanja mwa munthu wamkazi.”+ Atatero, Debora ananyamuka nʼkupita ndi Baraki ku Kedesi.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda,11/15/2003, tsa. 29
9 Debora anayankha kuti: “Tipitiradi limodzi. Koma ulemerero sukhala wako pa nkhondo imeneyi, chifukwa Yehova adzapereka Sisera mʼmanja mwa munthu wamkazi.”+ Atatero, Debora ananyamuka nʼkupita ndi Baraki ku Kedesi.+