Oweruza 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinangochitika kuti Hiberi Mkeni+ anasiyana ndi Akeni, ana a Hobabu mpongozi wa Mose+ ndipo anamanga tenti yake pafupi ndi mtengo waukulu ku Zaananimu, ku Kedesi.
11 Zinangochitika kuti Hiberi Mkeni+ anasiyana ndi Akeni, ana a Hobabu mpongozi wa Mose+ ndipo anamanga tenti yake pafupi ndi mtengo waukulu ku Zaananimu, ku Kedesi.