Oweruza 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zitatero Yehova anasokoneza Sisera,+ magaleta ake onse ankhondo komanso asilikali ake onse pamaso pa Baraki. Kenako Sisera anatsika mʼgaleta lake nʼkuyamba kuthawa wapansi. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Nsanja ya Olonda,8/1/2015, tsa. 1412/15/1998, ptsa. 11-125/1/1990, tsa. 17
15 Zitatero Yehova anasokoneza Sisera,+ magaleta ake onse ankhondo komanso asilikali ake onse pamaso pa Baraki. Kenako Sisera anatsika mʼgaleta lake nʼkuyamba kuthawa wapansi.