Oweruza 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Baraki anathamangitsa magaleta ankhondowo ndi asilikali onsewo mpaka ku Haroseti-ha-goimu. Asilikali onse a Sisera anaphedwa ndi lupanga moti sipanatsale ngakhale mmodzi.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:16 Nsanja ya Olonda,8/1/2015, tsa. 14
16 Baraki anathamangitsa magaleta ankhondowo ndi asilikali onsewo mpaka ku Haroseti-ha-goimu. Asilikali onse a Sisera anaphedwa ndi lupanga moti sipanatsale ngakhale mmodzi.+