Oweruza 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mvetserani mafumu inu. Inu olamulira, tcherani khutu. Ine ndidzaimbira Yehova. Ndidzaimba nyimbo zotamanda Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.+
3 Mvetserani mafumu inu. Inu olamulira, tcherani khutu. Ine ndidzaimbira Yehova. Ndidzaimba nyimbo zotamanda Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.+