Oweruza 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,Dziko linagwedezeka ndipo kumwamba kunagwetsa madzi,Mitambo inagwetsa madzi. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:4 Nsanja ya Olonda,8/1/2015, tsa. 14
4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,Dziko linagwedezeka ndipo kumwamba kunagwetsa madzi,Mitambo inagwetsa madzi.