Oweruza 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼmasiku a Samagara+ mwana wa Anati,Mʼmasiku a Yaeli,+ mʼnjira munalibe odutsamo,Ndipo anthu oyenda ankadutsa njira zolambalala. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda,8/1/2015, ptsa. 12-13
6 Mʼmasiku a Samagara+ mwana wa Anati,Mʼmasiku a Yaeli,+ mʼnjira munalibe odutsamo,Ndipo anthu oyenda ankadutsa njira zolambalala.