-
Oweruza 5:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mawu a anthu otunga madzi anamveka pamalo otungira madzi;
Kumeneko ankafotokoza ntchito zolungama za Yehova,
Ankafotokoza ntchito zolungama za anthu ake okhala mʼmidzi ya Isiraeli.
Kenako anthu a Yehova anapita kumizinda.
-