Oweruza 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amene anali mʼchigwa anachokera mʼfuko la Efuraimu,Akukutsatira iwe Benjamini, pakati pa anthu a mtundu wako. Atsogoleri a asilikali anachokera kwa Makiri,+Ndipo osunga zida za mlembi, anachokera mʼfuko la Zebuloni.
14 Amene anali mʼchigwa anachokera mʼfuko la Efuraimu,Akukutsatira iwe Benjamini, pakati pa anthu a mtundu wako. Atsogoleri a asilikali anachokera kwa Makiri,+Ndipo osunga zida za mlembi, anachokera mʼfuko la Zebuloni.