Oweruza 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Kenako mafumu a Kanani anamenya nkhondo;+Anamenya nkhondo ku Taanaki, pafupi ndi madzi a ku Megido.+ Iwo sanapezepo siliva woti atenge.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:19 Nsanja ya Olonda,8/1/2015, tsa. 14
19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Kenako mafumu a Kanani anamenya nkhondo;+Anamenya nkhondo ku Taanaki, pafupi ndi madzi a ku Megido.+ Iwo sanapezepo siliva woti atenge.+