-
Oweruza 5:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mngelo wa Yehova anati: ‘Tembererani Merozi,
Tembererani anthu ake,
Chifukwa sanathandize Yehova,
Sanabwere ndi anthu amphamvu kudzathandiza Yehova.’
-