Oweruza 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkazi wodalitsika kwambiri ndi Yaeli+Mkazi wa Hiberi Mkeni;+Ndi wodalitsika kwambiri pakati pa akazi onse okhala mʼmatenti. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:24 Nsanja ya Olonda,8/1/2015, tsa. 15
24 Mkazi wodalitsika kwambiri ndi Yaeli+Mkazi wa Hiberi Mkeni;+Ndi wodalitsika kwambiri pakati pa akazi onse okhala mʼmatenti.