Oweruza 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anatenga chikhomo cha tenti.Ndi dzanja lake lamanja anatenga hamala yolemera. Atatero anakhoma Sisera nʼkuphwanya mutu,Anaphwanya ndi kuboola fupa lapafupi ndi khutu.+
26 Kenako anatenga chikhomo cha tenti.Ndi dzanja lake lamanja anatenga hamala yolemera. Atatero anakhoma Sisera nʼkuphwanya mutu,Anaphwanya ndi kuboola fupa lapafupi ndi khutu.+