-
Oweruza 5:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Sisera anagwa nʼkugona pakati pa mapazi a Yaeli;
Pakati pa mapazi ake, iye anagwa nʼkugona;
Pamene anagwerapo, anagona pomwepo atagonja.
-