Oweruza 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu wamkazi anayangʼana pawindo,Amayi a Sisera anayangʼana pawindo ndipo anati,‘Nʼchifukwa chiyani galeta lake lankhondo likuchedwa kubwera? Nʼchifukwa chiyani mapazi a mahatchi a magaleta ake akuchedwa kumveka?’+
28 Munthu wamkazi anayangʼana pawindo,Amayi a Sisera anayangʼana pawindo ndipo anati,‘Nʼchifukwa chiyani galeta lake lankhondo likuchedwa kubwera? Nʼchifukwa chiyani mapazi a mahatchi a magaleta ake akuchedwa kumveka?’+