-
Oweruza 5:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 ‘Ayenera kuti akugawa zinthu zimene apeza,
Akugawa mtsikana mmodzi, kapena atsikana awiri kwa msilikali aliyense,
Nsalu zokongola za Sisera, ndithu nsalu zokongola,
Chovala chopeta chokongola, inde, zovala ziwiri zopeta,
Zoti amuna omwe alanda zinthu avale mʼmakosi awo.’
-