Oweruza 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe,+Koma amene amakukondani awale ngati mmene dzuwa limawalira likamatuluka.” Ndipo dzikolo linakhala pa mtendere kwa zaka 40.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:31 Nsanja ya Olonda,2/15/1986, ptsa. 21, 24 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 18
31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe,+Koma amene amakukondani awale ngati mmene dzuwa limawalira likamatuluka.” Ndipo dzikolo linakhala pa mtendere kwa zaka 40.+