Oweruza 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo ankabwera ndi ziweto zawo ndi matenti awo. Ankabwera ochuluka kwambiri ngati dzombe,+ ndipo iwo ndi ngamila zawo anali osawerengeka.+ Ankabwera mʼdzikomo nʼkumaliwononga.
5 Iwo ankabwera ndi ziweto zawo ndi matenti awo. Ankabwera ochuluka kwambiri ngati dzombe,+ ndipo iwo ndi ngamila zawo anali osawerengeka.+ Ankabwera mʼdzikomo nʼkumaliwononga.