Oweruza 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndinakupulumutsani kwa Aiguputo ndiponso kwa anthu onse amene ankakuponderezani, ndipo ndinawathamangitsa pamaso panu nʼkukupatsani dziko lawo.+
9 Choncho ndinakupulumutsani kwa Aiguputo ndiponso kwa anthu onse amene ankakuponderezani, ndipo ndinawathamangitsa pamaso panu nʼkukupatsani dziko lawo.+