Oweruza 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso ndinakuuzani kuti: “Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Musamalambire* milungu ya Aamori amene mukukhala mʼdziko lawo.”+ Koma inu simunamvere mawu anga.’”+
10 Komanso ndinakuuzani kuti: “Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Musamalambire* milungu ya Aamori amene mukukhala mʼdziko lawo.”+ Koma inu simunamvere mawu anga.’”+