Oweruza 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero, Yehova anamuyangʼana nʼkumuuza kuti: “Pita ndi mphamvu zimene uli nazozi, ndipo udzapulumutsa Isiraeli kwa Amidiyani.+ Kodi si ine amene ndakutuma?” Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:14 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, tsa. 16
14 Atatero, Yehova anamuyangʼana nʼkumuuza kuti: “Pita ndi mphamvu zimene uli nazozi, ndipo udzapulumutsa Isiraeli kwa Amidiyani.+ Kodi si ine amene ndakutuma?”