Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 6:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno Gidiyoni analowa mʼnyumba nʼkumuphera mwana wa mbuzi. Anatenganso ufa wokwana muyezo umodzi wa efa*+ nʼkupanga mikate yopanda zofufumitsa. Atatero, anatenga nyamayo nʼkuiika mʼbasiketi, ndipo msuzi anauika mumphika. Kenako anatenga zinthu zimenezi nʼkukamupatsa mngeloyo pansi pa mtengo waukulu uja.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena