Oweruza 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho, Gidiyoni anamangira Yehova guwa lansembe pamalowo, ndipo limatchedwa Yehova-salomu*+ mpaka pano. Guwalo lili ku Ofira, mzinda wa Aabi-ezeri, mpaka pano. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:24 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, ptsa. 22-23
24 Choncho, Gidiyoni anamangira Yehova guwa lansembe pamalowo, ndipo limatchedwa Yehova-salomu*+ mpaka pano. Guwalo lili ku Ofira, mzinda wa Aabi-ezeri, mpaka pano.