Oweruza 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Usiku womwewo, Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Tenga ngʼombe yaingʼono yamphongo ya bambo ako, ngʼombe yachiwiri yazaka 7 ija. Kenako ugwetse guwa lansembe la Baala la bambo ako ndipo udule mzati wopatulika* umene uli pafupi ndi guwalo.+
25 Usiku womwewo, Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Tenga ngʼombe yaingʼono yamphongo ya bambo ako, ngʼombe yachiwiri yazaka 7 ija. Kenako ugwetse guwa lansembe la Baala la bambo ako ndipo udule mzati wopatulika* umene uli pafupi ndi guwalo.+