-
Oweruza 6:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Choncho Gidiyoni anatenga amuna 10 pa atumiki ake ndi kuchita zonse zimene Yehova anamuuza. Koma chifukwa choti ankaopa kwambiri anthu amʼnyumba ya bambo ake ndi anthu a mumzindawo, anachita zimenezi usiku osati masana.
-