Oweruza 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zitatero, Gidiyoni anagwidwa ndi mzimu wa Yehova,+ moti analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndipo Aabi-ezeri+ anasonkhana pamodzi nʼkuyamba kumutsatira.
34 Zitatero, Gidiyoni anagwidwa ndi mzimu wa Yehova,+ moti analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndipo Aabi-ezeri+ anasonkhana pamodzi nʼkuyamba kumutsatira.