-
Oweruza 6:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Iye anatumiza uthenga kwa anthu amʼdera lonse la fuko la Manase, ndipo nawonso anasonkhana pamodzi nʼkuyamba kumutsatira. Anatumizanso uthenga mʼmadera onse a mafuko a Aseri, Zebuloni ndi Nafitali, ndipo nawonso anabwera kudzakumana naye.
-