-
Oweruza 6:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Ndipo zinachitikadi choncho. Atadzuka mʼmawa tsiku lotsatira nʼkufinya ubweya wa nkhosawo, ubweyawo unatulutsa madzi oti akhoza kudzaza mbale yolowa yaikulu.
-