-
Oweruza 6:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Choncho Mulungu anachitadi zimenezi usiku umenewo. Ubweya wokhawo unali wouma koma nthaka yonse inanyowa ndi mame.
-