Oweruza 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yerubaala,+ kapena kuti Gidiyoni, ndi anthu onse amene anali naye, anadzuka mʼmawa nʼkumanga msasa pa Kasupe wa Harodi. Msasa wa Amidiyani unali chakumpoto, mʼchigwa, kuphiri la More.
7 Kenako Yerubaala,+ kapena kuti Gidiyoni, ndi anthu onse amene anali naye, anadzuka mʼmawa nʼkumanga msasa pa Kasupe wa Harodi. Msasa wa Amidiyani unali chakumpoto, mʼchigwa, kuphiri la More.