Oweruza 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Anthu amene uli nawowa ndi ambiri kuti ndipereke Amidiyani mʼmanja mwawo,+ chifukwa Isiraeli angadzitame pamaso panga nʼkumanena kuti, ‘Ndinadzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.’+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, ptsa. 25-26
2 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Anthu amene uli nawowa ndi ambiri kuti ndipereke Amidiyani mʼmanja mwawo,+ chifukwa Isiraeli angadzitame pamaso panga nʼkumanena kuti, ‘Ndinadzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.’+