Oweruza 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano lengeza kwa anthu onse kuti, ‘Aliyense amene akuchita mantha kapena kunjenjemera abwerere kunyumba.’”+ Choncho Gidiyoni anayesa anthuwo ndipo anthu 22,000 anabwerera nʼkutsala anthu 10,000.
3 Tsopano lengeza kwa anthu onse kuti, ‘Aliyense amene akuchita mantha kapena kunjenjemera abwerere kunyumba.’”+ Choncho Gidiyoni anayesa anthuwo ndipo anthu 22,000 anabwerera nʼkutsala anthu 10,000.