-
Oweruza 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho Gidiyoni anauza anthuwo kuti apite kumadzi.
Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Aliyense amene akamwe madzi potunga madziwo ndi manja, ukamuike kumbali ina. Ndipo aliyense amene akamwe madzi atagwada nʼkuwerama, ukamuike kumbali inanso.”
-