-
Oweruza 7:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndipo anthu amene anamwa madzi ndi manja analipo 300. Koma ena onse anamwa atagwada nʼkuwerama.