Oweruza 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Ndidzakupulumutsani pogwiritsa ntchito amuna 300 amene amwa madzi ndi manja awo, ndipo ndidzapereka Amidiyani mʼmanja mwanu.+ Koma ena onsewo abwerere kunyumba.”
7 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Ndidzakupulumutsani pogwiritsa ntchito amuna 300 amene amwa madzi ndi manja awo, ndipo ndidzapereka Amidiyani mʼmanja mwanu.+ Koma ena onsewo abwerere kunyumba.”