Oweruza 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, iye anabweza amuna ena onse a Isiraeli nʼkutsala ndi amuna 300 aja. Iwo anatenga chakudya ndi malipenga a nyanga ya nkhosa kwa anthu amene ankabwererawo. Msasa wa Amidiyani unali kumunsi kwawo, mʼchigwa.+
8 Choncho, iye anabweza amuna ena onse a Isiraeli nʼkutsala ndi amuna 300 aja. Iwo anatenga chakudya ndi malipenga a nyanga ya nkhosa kwa anthu amene ankabwererawo. Msasa wa Amidiyani unali kumunsi kwawo, mʼchigwa.+