Oweruza 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukakafika, ukamvetsere zolankhula zawo. Ukakatero ukalimba mtima* ndipo udzapitadi kumsasawo kukamenyana nawo.” Kenako Gidiyoni ndi mtumiki wake Pura, anatsetserekera kumunsi pafupi kwambiri ndi asilikali amene anali mumsasawo.
11 Ukakafika, ukamvetsere zolankhula zawo. Ukakatero ukalimba mtima* ndipo udzapitadi kumsasawo kukamenyana nawo.” Kenako Gidiyoni ndi mtumiki wake Pura, anatsetserekera kumunsi pafupi kwambiri ndi asilikali amene anali mumsasawo.