Oweruza 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Gidiyoni atangomva malotowo ndi tanthauzo lake,+ analambira Mulungu. Kenako anabwerera kumsasa wa Isiraeli nʼkunena kuti: “Tiyeni, Yehova wapereka msasa wa Amidiyani mʼmanja mwanu.”
15 Gidiyoni atangomva malotowo ndi tanthauzo lake,+ analambira Mulungu. Kenako anabwerera kumsasa wa Isiraeli nʼkunena kuti: “Tiyeni, Yehova wapereka msasa wa Amidiyani mʼmanja mwanu.”