Oweruza 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako amuna a ku Efuraimu anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenyana ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anakangana naye kwambiri.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, tsa. 25
8 Kenako amuna a ku Efuraimu anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenyana ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anakangana naye kwambiri.+