-
Oweruza 8:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno iye anapempha amuna a ku Sukoti kuti: “Agawireni mkate anthu amene akunditsatirawa chifukwa atopa. Ndikuthamangitsa Zeba ndi Zalimuna, mafumu a Midiyani.”
-