-
Oweruza 8:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Gidiyoni atamva zimenezi anati: “Anali abale anga, ana a amayi anga. Ndikulumbira mʼdzina la Yehova, Mulungu wamoyo, mukanapanda kuwapha, inenso sindikanakuphani.”
-