-
Oweruza 8:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno anauza Yeteri mwana wake woyamba kuti: “Nyamuka uwaphe.” Koma mnyamatayo sanasolole lupanga lake chifukwa anachita mantha, poti anali adakali wamngʼono.
-