Oweruza 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako amuna a Isiraeli anauza Gidiyoni kuti: “Ukhale wolamulira wathu, iweyo, mwana wako ndi mdzukulu wako, chifukwa watipulumutsa kwa Amidiyani.”+
22 Kenako amuna a Isiraeli anauza Gidiyoni kuti: “Ukhale wolamulira wathu, iweyo, mwana wako ndi mdzukulu wako, chifukwa watipulumutsa kwa Amidiyani.”+