Oweruza 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Gidiyoni mwana wa Yowasi anamwalira atakalamba komanso atakhala ndi moyo wabwino, ndipo anamuika mʼmanda a Yowasi bambo ake, mumzinda wa Ofira wa Aabi-ezeri.+
32 Kenako Gidiyoni mwana wa Yowasi anamwalira atakalamba komanso atakhala ndi moyo wabwino, ndipo anamuika mʼmanda a Yowasi bambo ake, mumzinda wa Ofira wa Aabi-ezeri.+