-
Oweruza 9:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho azichimwene awo a mayi ake anakauza atsogoleri onse a Sekemu zimenezi, ndipo mitima yawo inayamba kutsatira Abimeleki, chifukwa anati: “Ndi mchimwene wathu ameneyu.”
-